Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
Ali m’ndende ku Eritrea, munthu wina anadzionela yekha kuti a Mboni amacita zimene amaphunzitsa ena mu umoyo wawo.
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > ANAKHALABE OKHULUPIRIKA ATAKUMANA NDI MAYESERO.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndingatani Kuti Ndisamapanikizike Kwambiri?
Dziŵani zimene zimabweletsa vutoli, na kudziŵa ngati muli nalo, komanso zimene mungacite.
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.