Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndingaphunzitse Bwanji Chikumbumtima Changa?
Cikumbumtima canu cimaonetsa makhalidwe amene muli nawo, komanso cingakuthandizeni kudziŵa umunthu wanu weni-weni. Kodi cimakamba ciani za imwe?
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.
TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO
Mkazi wokhulupilika Mariya Mmagadala anali mmodzi mwa ophunzila oyamba kuona Yesu ataukitsidwa. Anakhala na mwayi wouzako ena uthenga wabwino umenewu.
Pitani pa jw.org, ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO.