Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
M’busa ndi mkazi wake analila kwambili mwana wawo wamwamuna atamwalila cifukwa ca matenda. Koma posakhalitsa anapeza mayankho ogwila mtima a mafunso omwe anali nawo okhudza imfa.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA.
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO
Kodi Lamulo Lakuti “Diso Kulipira Diso” Limatanthauza Chiyani?
Kodi lamulo lakuti “diso kulipila diso” linkapeleka ufulu woti anthu azibwezelana?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO.