Zina Zimene Zilipo Pa JW.Org
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Patsiku loyamba kupita kunchito yake yatsopano, Michael Kuenzle anafunsidwa kuti, “Kodi ukuganiza kuti Mulungu ndi amene amacititsa mavuto padzikoli?” Apa m’pamene anasinthila umoyo wake.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi zipangizo zamakono zingathandize? Kodi kaonedwe kanu ka zinthu kangathandize?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.