Zamkatimu
ZA M’KOPE INO
Nkhani Yophunzila 22: August 2-8, 2021
2 Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kuti Akakhale Ophunzila Obatizika
Nkhani Yophunzila 23: August 9-15, 2021
8 Yehova Ali Namwe, Simuli Mwekha
Nkhani Yophunzila 24: August 16-22, 2021
14 Mungathe Kuwonjoka m’Misampha ya Satana!
Nkhani Yophunzila 25: August 23-29, 2021
25 Kodi Mudziŵa?—Kodi anthu m’nthawi ya Yesu anali kukhoma misonkho yotani?
26 Mbili Yanga—Pa Zonse Zimene Nimasankha, Nimaika Yehova Patsogolo