Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Kodi munthu amene anali bwana, anapeza bwanji cinthu camtengo wapatali kuposa cuma?
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.
ZIMENE ACINYAMATA AMAFUNSA
Mavuto amagwela munthu aliyense. Ndiye cifukwa cake tiyenela kukhala opilila, kaya mavutowo akhale aakulu bwanji.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti, LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZIMENE ACINYAMATA AMAFUNSA.