Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
ZOCITIKA
Mboni za Yehova ku Guatemala, zinalalikila anthu ambili okamba ci Kekchi.
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti LIBRARY > ARTICLE SERIES > EXPERIENCES OF JEHOVAH’S WITNESSES > SHARING BIBLE TRUTH.
KODI ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILITSIDWA NCHITO BWANJI?
Kacipangizo Kothandiza Kwambili
Tsopano Mboni za Yehova zambili zingacite daunilodi zofalitsa za pa cipangizo popanda kuseŵenzetsa Intaneti.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KODI ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILITSIDWA NCHITO BWANJI?