Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
EXPERIENCES OF JEHOVAH’S WITNESSES
A Blind Woman’s Prayers Are Answered
Mingjie anali kupemphela kuti akumane na Akhristu oona. N’ciani cinamupangitsa kuona kuti mapemphelo ake ayankhidwa?
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti LIBRARY > ARTICLE SERIES > EXPERIENCES OF JEHOVAH’S WITNESSES > SHARING BIBLE TRUTH.
FROM OUR ARCHIVES
Jehovah’s Witnesses in New Zealand—Peaceful and Devout Christians?
M’ma 1940, n’cifukwa ciani Mboni za Yehova zinali kuonedwa kuti ni anthu oopsa?
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti ARTICLE SERIES > FROM OUR ARCHIVES.