Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
Sukulu ya Giliyadi—Ophunzila Ake Amacokela Padziko Lonse
Ku New York kumacitika sukulu yofunika kwambili, koma ophunzila ake amacokela padziko lonse lapansi. Kodi ophunzila amayenda bwanji kuti akafike ku sukuluyi?
Pitani pa jw.org pa mbali yakuti, LAIBULALI > MPAMBO WA NKHANI > MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO.
THE BIBLE CHANGES LIVES
“Martial Arts Were My Passion”
Erwin Lamsfus anafunsa mnzake kuti, “Kodi unayamba waganizilapo cifukwa cake tili na moyo?” Yankho la funso limeneli linasintha umoyo wake.
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti, LIBRARY > ARTICLE SERIES > THE BIBLE CHANGES LIVES.