Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
Madzi Osefukira Anabweretsa Uthenga Wabwino
Midzi yosefukila na madzi ku Nicaragua inalandila thandizo pamene a Mboni za Yehova anaseŵenzetsa boti yawo kukapeleka thandizo la kuthupi na cilimbikitso cauzimu.
Pitani pa jw.org ku Chichewa pa mbali yakuti, LAIBULALI > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > KUUZA ENA CHOONADI CHA M’BAIBULO.
FROM OUR ARCHIVES
Kodi Mboni za Yehova zinathandiza bwanji Akhristu anzawo ku Germany pambuyo pa nkhondo yaciŵili ya padziko lonse?
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti, LIBRARY > ARTICLE SERIES > FROM OUR ARCHIVES.