Zina Zimene Zilipo Pa Jw.Org
MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
Amishonale Akutumizidwa “Mpaka Kumalekezelo a Dziko Lapansi”
Amishonale a m’munda oposa 3,000 akutumikila padziko lonse lapansi. Kodi ndalama zosamalila amishonale a m’munda amenewa zimacokela kuti?
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Zimene Mungacite Kuti Musamagwile Nchito Pamene Simuli Kunchito
Mfundo zisanu zimene zingakuthandizeni kuti nchito yanu isamasokoneze banja lanu.
NKHANI ZOKHUDZA MBONI ZA YEHOVA
N’cifukwa ciyani matica pa sukulu ina tsopano amachula Mboni za Yehova akamaphunzitsa za amene anazunzidwa kundende zacibalo za cipani ca Nazi?