LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp23 na. 1 masa. 1-2
  • Baibo Ingathandize Odwala Matenda a Maganizo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Baibo Ingathandize Odwala Matenda a Maganizo
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2023
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2023
wp23 na. 1 masa. 1-2
Nsanja ya Mlonda Na. 1 2023 | Baibo Ingathandize Odwala Matenda a Maganizo.

Baibo Ingathandize Odwala Matenda a Maganizo

Na. 1 2023

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa mwa zopeleka zaufulu. Kuti mucite copeleka, pitani pa donate.jw.org. Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.

MAGAZINI ya Nsanja ya Mlonda, imalemekeza Yehova Mulungu, amene ni Wolamulila wacilengedwe conse. Imalimbikitsa anthu na uthenga wabwino wakuti posacedwa Ufumu wa Mulungu udzacotsapo zoipa zonse, na kusintha dziko lapansi kukhala paradaiso. Imalimbikitsanso anthu kukhulupilila Yesu Khristu amene anatifela kuti tikapeze moyo wosatha. Ndipo pa nthawi ino, iye alamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magazini ino yakhala ikufalitsidwa kuyambila mu 1879, ndipo siloŵelela m’nkhani zandale. Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibo.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani