Yophunzila
JANUARY 2023
NKHANI ZOPHUNZILA: FEBRUARY 27–APRIL 2, 2023
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
LEMBA LA CAKA CA 2023:
“Mawu anu onse ndi coonadi cokha-cokha.” —SAL. 119:160
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PACIKUTO:
Akatswili okopolola Malemba Acihebeli anaonetsetsa kuti zimene anakopolola m’Mawu a Mulungu n’zolondola (Onani nkhani yophunzila 1, ndime 5)