Yophunzila
SEPTEMBER 2023
NKHANI ZOPHUNZILA: NOVEMBER 6–DECEMBER 10, 2023
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PACIKUTO:
Yehova anapatsa Samisoni mphamvu kuti akwanilitse nchito imene anam’patsa na kugonjetsa Afilisiti (Onani nkhani yophunzila 37, ndime 15)