LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w23 November masa. 1-32
  • Yophunzila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yophunzila
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
w23 November masa. 1-32
Ezara na a Aisiraeli ena akulila pakacisi. Ndiyeno Sekaniya akumuthandiza kuimilila.

Yophunzila

NOVEMBER 2023

NKHANI ZOPHUNZILA: JANUARY 8–FEBRUARY 4, 2024

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.

Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.

CITHUNZI CA PACIKUTO:

Ezara akupemphela uku akulila ali pa kacisi cifukwa ca macimo a anthu. Khamu la anthu nalonso likulila. Ndiyeno Sekaniya akulimbikitsa Ezara pomutsimikizila kuti: “Aisiraeli ali ndi ciyembekezo pa nkhani imeneyi . . . ndipo ife tili nawe.”—Ezara 10:​2, 4 (Onani nkhani yophunzila 48, ndime 17)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani