LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w23 December masa. 1-32
  • Yophunzila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yophunzila
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
w23 December masa. 1-32
Mlongo wacitsikana komanso m’bale wacinyamata mwacimwemwe akukula akhristu okhwima. Mlongoyo akusinkhasinkha atanyamula Baibo yake; M’bale akulalikila. Zithunzi: Abale na alongo acicepele okhwima mwauzimu akutengamo mbali mu nchito za gulu. 1. Mlongo akukonza thebulo m’cipinda codyela pa Beteli. 2. Alongo aŵili akuŵelengela lemba mzimayi mu ulaliki. 3. Mlongo akucita ulaliki wa pa kasitandi na mlongo wacikulile. 4. M’bale akuphunzitsa m’bale wacikulile mmene angaseŵenzetsele tabuleti yake. 5. M’bale akuŵelenga Baibo ku pulatifomu pa msonkhano wa mpingo. 6. M’bale akugwila nchito pa cimango.

Yophunzila

DECEMBER 2023

NKHANI ZOPHUNZILA: FEBRUARY 5–MARCH 3, 2024

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.

Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.

CITHUNZI CA PACIKUTO:

Anyamata na atsikana ambili amene anaphunzitsidwa Malemba na kugwilitsa nchito zimene anaphunzila, akhala Akhristu okhwima (Onani nkhani yophunzila 52, ndime 21, komanso nkhani yophunzila 53, ndime 19-20)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani