Yophunzila
JANUARY 2024
NKHANI ZOPHUNZILA: MARCH 4–APRIL 7, 2024
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
LEMBA LA CAKA CA 2024:
“Ine ndidzadalila inu, tsiku lililonse limene ndingacite mantha.”—SAL. 56:3.
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.