LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w24 September masa. 1-32
  • Yophunzila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yophunzila
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
w24 September masa. 1-32
Yesu wakhala pa mpando wacifumu kumwamba ndipo akuona zocita za magulu aŵili a anthu. Zithunzi: Abale na alongo akulambila Yehova. 1. Mlongo ali na tabuleti m’manja ndipo akuyang’ana kumwamba. 2. Mwamuna na mkazi wake akuŵelenga Baibo. 3. Abale na alongo akugwila nchito zomanga-manga za gulu. 4. M’bale akupemphela ali m’ndende. 5. Mlongo wacikulile akupeleka ndemanga pa msonkhano. 6. Mlongo wogonekedwa m’cipatala, akupatsa nesi kathilakiti. 7. Tate akuŵelenga cofalitsa na banja lake. Zithunzi: Amuna na akazi akucita zinthu zosemphana na mfundo za m’Baibo. 1. Mwamuna akupemphela m’malo ochailamo njuga. 2. Mwamuna akumenya mkazi. 3. Anthu okwiya akucita cionetselo. 4. Mwamuna wa mfuti akulondola mkazi ku malo oimikako mamotoka. 5. Mtsogoleli wa cipembedzo akupemphelela asilikali. 6. Mkazi akuseŵenzetsa mankhwala osokoneza bongo.

Yophunzila

SEPTEMBER 2024

NKHANI ZOPHUNZILA: NOVEMBER 11–DECEMBER 8, 2024

© 2024 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.

Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani