Zamkatimu
ZA M’KOPE INO
Nkhani Yophunzila 44: January 6-12, 2025
2 Zimene Zingatithandize Kupilila Zopanda Cilungamo
Nkhani Yophunzila 45: January 13-19, 2025
8 Zimene Tiphunzilapo pa Mawu Othela Omwe Amuna Okhulupilika Anakamba
Nkhani Yophunzila 46: January 20-26, 2025
14 Abale—Kodi Mukuyesetsa Kuti Mukayenelele Kukhala Mtumiki Wothandiza?
Nkhani Yophunzila 47: January 27, 2025–February 2, 2025
20 Abale—Kodi Mukuyesetsa Kuti Mukayenelele Kukhala Mkulu?
26 Mbili Yanga—Yehova Anatipatsa Nyonga Panthawi ya Nkhondo Komanso ya Mtendele
31 Zimene Zingakuthandizeni Kucita Phunzilo la Munthu Mwini Mokhazikika
32 Mfundo Yothandiza pa Kuŵelenga Kwanu—Pezani Malo Abwino Oŵelengela