LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 100
  • Ndife Gulu Lankhondo la Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndife Gulu Lankhondo la Yehova
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Ndife Asilikali a Yehova!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Musaleke Kugwila Nchito, Kuyang’anila, na Kuyembekezela
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Imbirani Yehova
sn nyimbo 100

Nyimbo 100

Ndife Gulu Lankhondo la Yehova

(Yoweli 2:7)

1. Ndife gulu lankhondo

Lolalikira

Ufumu wa Mulungu.

Ukulamulira.

Timapitabe ndithu

Modzipereka.

Ndife osaopa

Olimba mtima.

(KOLASI)

Ndife gulu lankhondo.

Tikulengeza:

“Ufumu wayamba

Kulamulira.”

2. Ndife anthu a M’lungu

Ofunafuna

Anthu ongadi nkhosa

Omwe asochera.

Tifuna kuwapeza,

N’kuwaphunzitsa,

N’kuwalimbikitsa:

“Tizisonkhana.”

(KOLASI)

Ndife gulu lankhondo.

Tikulengeza:

“Ufumu wayamba

Kulamulira.”

3. Gululi n’la Yehova

N’lokonzekera

Kumenya nkhondo ndithu,

Molimbadi mtima.

Koma tikhale tcheru

Kuti tisagwe.

Zinthu zikavuta

Tisafooke.

(KOLASI)

Ndife gulu lankhondo.

Tikulengeza:

“Ufumu wayamba

Kulamulira.”

(Onaninso Afil. 1:7; Aef. 6:11, 14; Filim. 2.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani