LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 93
  • “Onetsani Kuwala Kwanu”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Onetsani Kuwala Kwanu”
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • “Onetsani Kuwala Kwanu”
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • “Onetsani Kuwala Kwanu” Kuti Yehova Alemekezeke
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
Imbirani Yehova
sn nyimbo 93

Nyimbo 93

“Onetsani Kuwala Kwanu”

(Mateyu 5:16)

1. Yesu walamula kuti tiwale,

Ngati dzuwa kuti onse aone.

Mawu a Mulungu apatsa nzeru.

Tionetse kuwala ndi ntchito zathu.

2. Uthenga wabwino umawalitsa

Mitima ya anthu, n’kuwatonthoza.

Kuwala kwa Mawu a M’lungu wathu

Kumatitsogolera mu ntchito yathu.

3. Dziko limawala ndi mawu athu,

Limawalirabe ndi ntchito zathu.

Pochita zabwino tidzawalabe.

Mulungu pomaona asangalale.

(Onaninso Sal. 119:130; Mat. 5:14, 15, 45; Akol. 4:6.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani