LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • ll gao 8 masa. 18-19
  • Kodi Timapindula Bwanji ndi Imfa ya Yesu?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Timapindula Bwanji ndi Imfa ya Yesu?
  • Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
  • Nkhani Zofanana
  • Gao 8
    Mvetselani kwa Mulungu
  • Kodi Ufumu Wa Mulungu N’ciani?
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Kodi Ufumu wa Mulungu N’ciani?
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
  • Akufa Adzauka Ndithu!
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
Onaninso Zina
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
ll gao 8 masa. 18-19

GAO 8

Kodi Timapindula Bwanji ndi Imfa ya Yesu?

Yesu anafa kuti tikapeze moyo. Yohane 3:16

Azimayi ayang’ana m’manda a Yesu opanda kanthu

Patapita masiku atatu kucokela pamene Yesu anafa, akazi ena anapita kumanda amene anamuikamo ndipo anapeza mulibe. Iwo anapeza kuti Yehova waukitsa Yesu kwa akufa.

Yesu aonekela kwa atumwi ake, kenako apita kumwamba

Pambuyo pake Yesu anaonekela kwa atumwi ake.

Inde, Yehova anaukitsa Yesu kukhala mngelo wamphamvu, amene sakhoza kufa. Ophunzila ake anamuona akupita kumwamba.

  • Kodi “malipilo” a uchimo n’ciani?—Aroma 6:23.

  • Yesu anatsegula njila ya kumoyo wamuyaya.—Aroma 5:21.

Mulungu anaukitsa Yesu ndi kumuika kukhala Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Danieli 7:13, 14

Yesu ali pa mpando wacifumu mu Ufumu wa Mulungu, akulamulila anthu m’paladaiso pa dziko lapansi

Yesu anapeleka moyo wake kukhala dipo la anthu onse. (Mateyu 20:28) Cifukwa ca dipo limenelo, Mulungu watipatsa mwai wakuti tikhale ndi moyo wamuyaya.

Yehova anasankha Yesu kukhala Mfumu ya dziko lapansi. Iye adzalamulila pamodzi ndi anthu okhulupilika okwanila 144,000 amene amaukitsidwa kucoka padziko kupita kumwamba. Yesu ndi a 144,000 amapanga boma la kumwamba lolungama—Ufumu wa Mulungu.—Chivumbulutso 14:1-3.

Ufumu wa Mulungu udzasandutsa dziko lapansi kukhala paladaiso. Nkhondo, upandu, kusauka, ndi njala zidzatha. Anthu adzakondwela kwambili.—Salimo 145:16.

  • Kodi Ufumu wa Mulungu uzabweletsa madalitso ati?—Salimo 72.

  • Tizipemphelela Ufumu wa Mulungu kuti ubwele.—Mateyu 6:10.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani