Maphunzilo amene tingatengemo m’Baibo
KUCOKELA M’NKHANI IZI
Acicepele, tumikilani Yehova na mtima wonse 37, 51, 59, 61, 72, 100
Anthu oipa sadzakhalakonso 5, 10, 32, 46, 102
Anthu onse ni ofunika kwa Yehova 8, 9, 11, 21, 23, 68, 70, 74, 87, 90
Anthu opanduka amakhala adani a Mulungu 7, 17, 26, 27, 28, 88
Cifunilo ca Mulungu cicitike kumwamba na pa dziko lapansi 25, 55, 60, 62, 63, 71, 96, 102
Kudzikonda kungativulaze ife, na kuvulazanso anthu ena 3, 4, 12, 27, 28, 39, 49, 88
Kulambila konama kumacokela kwa Satana 19, 20, 22, 38, 46, 49, 52, 58
Limbani mtima, Yehova adzakuthandizani nthawi zonse 40, 47, 51, 53, 57, 61, 64, 65, 76, 88, 101
Mabwenzi abwino koposa ni amene amakonda Yehova 16, 33, 42, 80, 87, 100, 103
Mkwiyo ni woipa 4, 12, 41, 45, 49, 65, 89
Moyo wanu umadalila pa kukhala womvela 3, 5, 10, 37, 39, 54, 59, 65, 72
Mulungu anatipatsa Baibo kuti tikhale anzelu 56, 66, 72, 75, 81
Musataye mtima pokumana na mavuto 16, 47, 51, 57, 64, 75, 90, 95, 99, 101
Muzikhululukila ena mmene Yehova amacitila kwa imwe 13, 15, 31, 43, 92
Muzikwanilitsa malonjezo anu mmene Yehova amacitila 8, 9, 11, 23, 24, 31, 34, 35, 36, 66, 93
Muziyamikila Yehova nthawi zonse 2, 6, 67, 103
Ngati simukonda m’bale wanu, simungakonde Mulungu 4, 13, 15, 41
Nsanje imawononga ubwenzi 4, 14, 41
Pangani Yehova kukhala bwenzi lanu 11, 30, 33, 51, 56, 59, 69, 81, 82
Pewani kucita zoipa 14, 27, 49, 53, 58, 88, 89
Sitingatumikile Mulungu na Cuma pa nthawi imodzi 10, 17, 44, 59, 75, 76
Tetezani zimene Yehova wakupatsani 12, 13, 24, 35, 36, 56, 75, 95, 100
Tifunika kulalikila uthenga wabwino wa Ufumu 73, 76, 94, 95, 96, 97, 98
Ufumu wa Mulungu udzabweletsa cimwemwe kwa aliyense 1, 48, 62, 79, 81, 83, 85, 86
Yehova amakonda anthu a mitundu yonse 30, 33, 48, 54, 77, 94, 97, 98, 99
Yehova amamvela mapemphelo athu ocokela pansi pa mtima 35, 38, 50, 64, 82
Yehova amateteza anthu amene amam’konda 6, 22, 40, 50, 52, 55, 64, 71, 84
Yehova amateteza anthu odzicepetsa 43, 45, 65, 67, 69
Yehova amatsogolela anthu ake 18, 25, 26, 27, 29, 34, 39, 44, 73, 80
Yehova anatipangila dziko lapansi kuti tikhalepo 1, 2, 102, 103
Yehova ni wamphamvuzonse 1, 7, 18, 19, 20, 21, 22, 26, 55, 60
Yehova sanama 3, 10, 16, 63, 68, 70, 102, 103
Yehova sangaiŵale zimene timam’citila 16, 29, 32, 48, 65, 69, 77, 100
Yesu ni Mfumu ya Ufumu wa Mulungu—mumveleni 74, 78, 79, 83, 84, 85, 91, 92, 99