LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • CA-brpgm20 tsa. 4
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
  • 2019-2020 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woimila Nthambi
  • Nkhani Zofanana
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
    2019-2020 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
  • Pezani Mayankha pa Mafunso Awa
    2022-2023 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
    2020-2021 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woyang’anila Dela
  • Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
    2023-2024 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woimila Nthambi
Onaninso Zina
2019-2020 Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela—Wa Woimila Nthambi
CA-brpgm20 tsa. 4

Pezani Mayankho Pa Mafunso Aya:

  1. Kodi tingaonetse bwanji cikondi cathu pa Mulungu? (Deut. 13:3, 4; 1 Yoh. 5:3)

  2. N’cifukwa ciani tifunika kukonda abale athu? (1 Yoh. 4:11, 20, 21)

  3. Kodi tingaonetse bwanji cikondi pa anthu anzathu? (Lev. 19:18; Aef. 5:29)

  4. Kodi tingaonetse bwanji kuti timatengela cikondi ca Yehova? (1 Pet. 4:8; Akol. 3:13)

  5. N’ciani cingatithandize kutamanda Yehova? (Sal. 104:33; 146:2, 5)

  6. Kodi kukonda Yehova na mtima wathu wonse kumatanthauza ciani? (Eks. 34:14; Amosi 5:15; Aroma 12:11)

© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani