LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 158
  • “Silidzacedwa!”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Silidzacedwa!”
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mudzayembekezela Moleza Mtima?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Khalanibe Oleza Mtima
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Kodi Mudzayembekezela Yehova Moleza Mtima?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Pezani Cimwemwe Poyembekezela Yehova Moleza Mtima
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 158

NYIMBO 158

“Silidzacedwa!”

Yopulinta

(Habakuku 2:3)

  1. 1. Dziko lapansi

    n’lokongoladi!

    Munalilenga

    mwa luso kwambili.

    Ngakhale kuti

    dziko lasintha

    Mudzalikonza

    kukhala labwino.

    (KOLASI)

    Tikulakalaka

    dziko latsopano.

    Tilezetseni mtima.

    Tsiku lanu M’lungu

    lidzafika ndithu.

    Olo litenge nthawi,

    Silidzacedwa!

  2. 2. Tiyembekeza

    nthawi imene

    Mudzaukitsa

    ogona mu imfa.

    Tidziŵa kuti

    mumaŵakonda.

    Tithandizeni

    tilezebe mtima.

    (KOLASI)

    Tikulakalaka

    dziko latsopano.

    Tilezetseni mtima.

    Tsiku lanu M’lungu

    lidzafika ndithu.

    Olo litenge nthawi,

    Silidzacedwa!

  3. 3. Moleza mtima

    mumapeleka

    Ciyembekezo

    kwa oona mtima.

    Polalikila

    mutithandiza,

    Timakondwela

    kukuyandikani.

    (KOLASI)

    Tikulakalaka

    dziko latsopano.

    Tilezetseni mtima.

    Tsiku lanu M’lungu

    lidzafika ndithu.

    Olo litenge nthawi

    Silidzacedwa!

    Tilezetseni mtima.

(Onaninso Akol. 1:11.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani