Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
1. N’cifukwa ciyani ‘siticita manyazi na uthenga wabwino’? (Aroma 1:16; 11:13)
2. Kodi timakhalila kumbuyo uthenga wabwino motani? (Mat. 10:32; Aroma 10:9)
3. Kodi n’ciyani cimatithandiza kukhala aluso mu utumiki? (2 Tim. 2:15)
4. Kodi tingatengele bwanji citsanzo ca Onesiforo? (2 Tim. 1:7, 8)
5. Kodi timaonetsa bwanji kuti siticita naye manyazi Mulungu wathu? (Aheb. 10:39; 1 Pet. 3:15; Yoh. 18:36; 1 Ates. 5:12, 13)
6. Kodi ‘timadzitamandila mwa Yehova’ m’njila yotani? (Sal. 34:1, 2; 1 Akor. 1:31)
© 2024 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-brpgm25-CIN