LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • PHUNZITSANI COONADI
  • Lemba: Yoh. 11:11-14
  • KAPEPA KOITANILA ANTHU KU MISONKHANO (inv)
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Funso:
  • Lemba:
  • Cogaŵila:
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 October tsa. 1
Mboni za Yehova zigaŵila kapepa koitanila ku misonkhano

Kuitanila anthu ku misonkhano

Maulaliki a Citsanzo

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 5 2016 | Kodi Nkhani Yonena za Yesu Ndi Yongopeka?

Funso: Anthu ena amakayikila kuti Yesu analiko, koma ena amakhulupilila kuti analikodi. Enanso amati palibe amene angadziŵe. Nanga inu muganiza bwanji?

Cogaŵila: Magazini iyi ya Galamukani! ifotokoza maumboni oonetsa kuti Yesu analikodi.

PHUNZITSANI COONADI

Baibo yotsegula

Funso: N’ciani cimacitika munthu akafa?

Lemba: Yoh. 11:11-14

Mfundo ya Coonadi: Munthu akafa, moyo wake umathela pamenepo. Ndipo sitifunika kuopa zimene zidzacitike tikadzafa. Yesu anayelekezela imfa ndi tulo. Monga mmene anaukitsila Lazaro, Yesu “adzaukitsa” okondedwa athu amene anafa kuti akasangalale na moyo pa dziko lapansi.—Yobu 14:14.

KAPEPA KOITANILA ANTHU KU MISONKHANO (inv)

Kapepa Koitanila ku Misonkhano

Cogaŵila: Mukuitanidwa ku nkhani ya m’Baibulo. Nkhani imeneyi idzakambidwa ku Nyumba ya Ufumu, malo athu olambilila. [M’patseni kapepa ka ciitano, ndipo muonetseni nthawi na malo a misonkhano ya kumapeto kwa mlungu. Muuzeni mutu wa nkhani ya anthu onse.]

Funso: Kodi munafikapo kale pa Nyumba ya Ufumu? [Ngati n’kotheka, muonetseni vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu?]

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani