LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsa. 2
  • “Khulupilila Yehova ndi Mtima Wako Wonse”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Khulupilila Yehova ndi Mtima Wako Wonse”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mumakhulupilila Mmene Yehova Amacitila Zinthu?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Khalani ndi Cikhulupililo Ndipo Muzipanga Zosankha Mwanzelu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Miyambo 3:5, 6—“Usamadalile Luso Lako Lomvetsa Zinthu”
    Kufotokoza Mavesi a m’Baibulo
  • Kodi Mumasankha Bwanji Zocita?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 October tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MIYAMBO 1–6

“Khulupilila Yehova ndi Mtima Wako Wonse”

Munthu wa m’nthawi yakale apemphela

Yehova ni woyenela kumukhulupilila ndi mtima wonse. Tanthauzo la dzina lake limatipangitsa kukhulupilila kuti adzakwanilitsa malonjezo ake onse. Pemphelo limatithandiza kwambili kukhulupilila Mulungu. Miyambo caputa 3 imatitsimikizila kuti, ngati ndife okhulupilika kwa Yehova, iye adzatidalitsa mwa ‘kuwongola njila zathu.’

Munthu amene amadziona kuti ni wanzelu . . .

3:5-7

  • amasankha zocita asanapemphe Yehova kuti amutsogolele

  • amadalila nzelu zake kapena za dziko

Munthu amene amakhulupilila Yehova . . .

  • amayesetsa kukhala pa ubwenzi wolimba ndi Mulungu mwa kuphunzila Baibo, kusinkha-sinkha, ndi kupemphela

  • amafuna-funa citsogozo ca Mulungu mwa kufufuza mfundo za m’Baibo pamene asankha zocita

PA MBALI ZIŴILI IZI, KODI INE NIMASANKHA BWANJI ZOCITA?

COYAMBA: Nimasankha zimene naona kuti ndiye zoyenela

COYAMBA: Nimapempha citsogozo ca Yehova kupitila m’pemphelo ndi phunzilo laumwini

CACIŴILI: Nimapempha Yehova kuti adalitse zimene nasankha

CACIŴILI: Nimapanga zosankha zogwilizana na mfundo za m’Baibo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani