CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YEREMIYA 29-31
Yehova Ananenelatu za Pangano Latsopano
Yopulinta
Yehova anakambilatu kuti pangano la Cilamulo lidzaloŵedwa m’malo na pangano latsopano limene lidzabweletsa mapindu amuyaya.
PANGANO LA CILAMULO |
PANGANO LATSOPANO |
|
---|---|---|
Yehova ndi Aisiraeli obadwila |
OLOŴETSEDWAMO |
Yehova ndi Isiraeli wauzimu |
Mose |
MKHALAPAKATI |
Yesu Khristu |
Nsembe za nyama |
LINATHEKA NDI |
Nsembe ya Yesu |
Pamagome amiyala |
LINALEMBEDWA PA |
M’mitima ya anthu |