CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZEKIELI 24-27
Ulosi wa Kuwonongedwa kwa Mzinda wa Turo Umalimbitsa Cidalilo m’Mau a Yehova
Yopulinta
Buku la Ezekieli linakambilatu tsatane-tsatane wa kuwonongedwa kwa mzinda wa Turo.
26:7-11
Patapita kanthawi pambuyo pa caka ca 607?B.C.E., n’ndani anawononga mzinda wa Turo?
26:4, 12
Mu 332 B.C.E., n’ndani anaseŵenzetsa zogumuka za mzinda wa Turo pokonza njila kuti akawononge cisumbu ca mzinda wa Turo?