CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZEKIELI 35-38
Gogi wa Magogi Adzawonongedwa Posacedwa
Baibo imafotokoza zimene zidzacitika Gogi wa Magogi asanawonongedwe na pambuyo pake.
Chiv. 17:16-18
Cisautso cacikulu cidzayamba na kuwonongedwa kwa
Ezek 38:2, 11, 15
Anthu a Yehova adzaukilidwa na
Chiv. 16:16
Yehova adzawononga Gogi wa Magogi pa nkhondo ya
Chiv. 20:4
Khristu adzayamba ulamulilo wake wa
Ningakonzekele bwanji mwauzimu za kuukilidwa ndi Gogi wa Magogi?