CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZEKIELI 39-41
Mmene Masomphenya a Ezekieli a Kacisi Amakukhudzilani
40:10, 14, 16
Zipinda za alonda na zipilala zazitali zitikumbutsa kuti miyezo ya Yehova ya kulambila koyela ni yapamwamba maningi
Dzifunseni kuti, ‘Ningasunge bwanji miyezo ya Yehova yapamwamba ndi yolungama?’