LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 January tsa. 1
  • Makambilano a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makambilano a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • ●○○ ULENDO WOYAMBA
  • ○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
  • ○●○ ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
  • Moseŵenzetsela Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mmene Tingaseŵenzetsele Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 January tsa. 1
Agaŵila kapepa ka uthenga pafupi na mzinda wa Monrovia, ku Liberia

Alalikila pafupi na mzinda wa Monrovia, ku Liberia

Makambilano a Citsanzo

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi Baibo ikali yothandiza masiku ano?

Lemba: 2 Tim. 3:16

Ulalo: Kodi m’Baibo muli uthenga wotani?

○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA

Funso: Kodi m’Baibo muli uthenga wotani?

Lemba: Mat. 6:10

Ulalo: Kodi Ufumu wa Mulungu udzacita ciani?

○●○ ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzacita ciani?

Lemba: Dan. 2:44

Ulalo: Kodi zimenezi zidzakhudza bwanji dziko lapansi?

Kuyambila mwezi uno, msonkhano wa mkati mwa wiki suzikhalanso na mbali zitatu za maulaliki a citsanzo. M’malomwake, Kabuku ka Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu, kadzayamba kukhala na makambilano a citsanzo, amene azikhala na funso loyambila makambilano, lemba, na funso lopanga ulalo ku ulendo wobwelelako. Wiki iliyonse, tizitamba vidiyo imodzi cabe ya makambilano a citsanzo. Wofalitsa aliyense angasankhe buku limodzi pa mabuku amene timaseŵenzetsa pophunzitsa anthu Baibo. Ndipo angaone pamene angaliseŵenzetse—kaya pa ulendo woyamba kapena wobwelelako. Ndiponso, kabukuka kazikhala na zitsanzo za makambilano. Njila ya makambilano imeneyi idzatithandiza kuika maganizo pa colinga cathu ca kuphunzitsa “onse amene [ali] ndi maganizo abwino . . . kukapeza moyo wosatha.”—Mac. 13:48.

Nkhani za Am’sukulu: Am’sukulu ndiwo afunika kucita makambilano a citsanzo, kupatulapo ngati pangakhale malangizo ena.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani