CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIKO 1-2
“Macimo Ako Akhululukidwa”
Tiphunzilapo ciani pa cozizwitsa ici?
- Kudwala kunabwela kaamba ka ucimo 
- Yesu ali na mphamvu zokhululukila macimo na kucilitsa odwala 
- Mu Ufumu wa Mulungu, Yesu adzacotsa ucimo na matenda kwamuyaya 
Kodi lemba la Maliko 2:5-12 linganithandize bwanji kupilila nikadwala?