CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 9-10
Yesu Amasamalila Nkhosa Zake
M’busa amakhala pa ubwenzi wabwino na nkhosa zake cifukwa ca kudziŵana na kukhulupililana. Yesu, amene ni M’busa Wabwino, amadziŵa nkhosa iliyonse payokha—zimene imasoŵeka, zofooka zake, komanso mphamvu zake. Nkhosa zimamudziŵa m’busa wawo, ndipo zimakhulupilila utsogoleli wake.
Ni motani mmene Yesu, M’busa Wabwino, . . .
amasonkhanitsila nkhosa zake?
amatsogolela nkhosa zake?
amatetezela nkhosa zake?
amadyetsela nkhosa zake?