LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 November tsa. 3
  • Mzimu Woyela Unatsanulidwa pa Mpingo Wacikhristu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mzimu Woyela Unatsanulidwa pa Mpingo Wacikhristu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Apatsidwa Mlandu Wakuti ni Wovutitsa Komanso Woukila Boma
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Paulo Apempha Kukaonekela kwa Kaisara Kenako Alalikila Mfumu Herode Agiripa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 November tsa. 3

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 1-3

Mzimu Woyela Unatsanulidwa pa Mpingo Wacikhristu

Khamu la anthu ocokela m’mitundu yosiyana-siyana ku Yerusalemu pa Pentekosite mu 33 C.E.

2:1-8, 14, 37, 38, 41-47

Ayuda ambili amene anali ku Yerusalemu pa Pentekosite wa mu 33 C.E. anali ocokela ku mitundu ina. (Mac. 2:9-11) Ngakhale kuti iwo anali kusunga Cilamulo ca Mose, ayenela kuti anakhala m’dziko lacilendo kwa umoyo wawo wonse. (Yer. 44:1) Conco, kaonekedwe na kakambidwe ka ena kayenela kuti kanali kuonetsa kuti sanali Ayuda. Anthu okwana 3,000 ocoka m’mitundu yosiyana-siyana atabatizidwa, mpingo wacikhristu unakhala na anthu okamba zitundu zosiyana-siyana. Olo kuti anali osiyana zikhalidwe, “anali kusonkhana kukacisi mogwilizana.”—Mac. 2:46.

Mungaonetse bwanji cikondi kwa . . .

  • anthu a m’gawo lanu amene anacokela ku madela ena?

  • abale na alongo a mu mpingo mwanu amene anacokela ku madela ena?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani