LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 December tsa. 4
  • Cigamulo Cozikidwa pa Mawu a Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Cigamulo Cozikidwa pa Mawu a Mulungu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Bungwe Lolamulila Limagwilila Nchito Masiku Ano
    Ndani Amene Akucita Cifunilo Ca Yehova Masiku Ano?
  • N’ndani Akutsogolela Anthu a Mulungu Masiku Ano?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Udindo wa “Kapolo Wokhulupilika ndi Wanzelu”
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Yehova Akutsogolela Gulu Lake
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 December tsa. 4
Mpingo wa m’nthawi ya atumwi umvetsela pamene cigamulo cocokela ku bungwe lolamulila cikuŵelengedwa

Mpingo umvetsela cigamulo cocokela ku bungwe lolamulila

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 15-16

Cigamulo Cozikidwa pa Mawu a Mulungu

Tiphunzilapo ciani pa mmene nkhaniyi anaisamalila?

15:1, 2—Tifunika kukhala odzicepetsa komanso oleza mtima. Paulo na Baranaba sanasamalile nkhaniyo paokha, m’malomwake anafunsila citsogozo ca gulu la Yehova.

15:28, 29—Tizikhulupilila gulu la Mulungu. Mpingo unali na cidalilo cakuti Yehova adzatsogolela pa nkhaniyo mwa kuseŵenzetsa mzimu wake woyela na Khristu Yesu.

16:4, 5—Tizikhala omvela. Cifukwa cotsatila citsogozo cocokela ku bungwe lolamulila, mpingo unapitiliza kukula.

Ni citsanzo cimodzi citi ca citsogozo cimene tinalandila posacedwapa kucokela ku gulu la Yehova?

Ningapindule bwanji ngati nimacitsatila?

Mpingo umvetsela cigamulo cocokela ku bungwe lolamulila

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani