LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 June tsa. 5
  • “Valani Zida Zonse Zankhondo Zocokela kwa Mulungu”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Valani Zida Zonse Zankhondo Zocokela kwa Mulungu”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 June tsa. 5
Munthu wavala zida zonse za nkhondo

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AEFESO 4-6

“Valani Zida Zonse Zankhondo Zocokela kwa Mulungu”

6:11-17

Mtumwi Paulo anayelekezela Akhristu na asilikali amene ali pa nkhondo. Adani athu ni “makamu a mizimu yoipa.” Koma olo tioneke ngati ofooka komanso osatetezeka, Yehova angatithandize kupambana pa nkhondoyi, malinga ngati tavala “zida zonse zankhondo zocokela kwa Mulungu.”

Chulani dzina la cida ciliconse ca nkhondo, na kufotokoza zimene cimaimila

Zida za nkhondo ciliconse pacokha-pacokha

ZOFUNIKA KUSINKHA-SINKHA: Kodi ndavala zida zonse za nkhondo?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani