CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 TIMOTEYO 4-6
Kudzipeleka kwa Mulungu Kapena ku Cuma
6:6-10
Kodi malemba otsatilawa, aonetsa bwanji kuti tingakhale acimwemwe kwambili ngati tadzipeleka kwa Mulungu m’malo mofuna-funa cuma?
Anthu amene amayamba utumiki wa nthawi zonse amapeza madalitso
Mlal. 5:10
Mlal. 5:12
N’cifukwa ciani n’zosatheka kucita zonse ziŵili panthawi imodzi, kudzipeleka kwa Mulungu komanso ku Cuma? (Mat. 6:24)