CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YAKOBO 1-2
Zimene Zimabweletsa Macimo na Imfa
1:14, 15
Ngati mwayamba kuganizila zinthu zolakwika, citani izi:
Yambani kuganizila zinthu zina zabwino.—Afil. 4:8
Ganizilani mavuto amene mungakumane nawo ngati mwagonja ku ciyeselo.—Deut. 32:29
Pemphelani.—Mat. 26:41
izila zinthu zolakwika, ni zinthu zolimbikitsa ziti zimene mungaganizile m’malomwake?