CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | CHIVUMBULUTSO 13-16
Musamaope Zilombo Zoopsa
13:1, 2, 11, 15-17
Kumvetsetsa zimene zilombo zochulidwa mu Chivumbulutso caputa 13 zimaimila, kumatithandiza kupewa kuziyopa kapena kuzikhumbila na kuzicilikiza monga mmene anthu ena amacitila.
GWILIZANITSANI CILOMBO CILICONSE NA ZIMENE CIIMILA
ZILOMBO
Cinjoka.—Chiv. 13:, ftn.
Cilombo ca nyanga 10 na mitu 7.—Chiv. 13:1, 2
Cilombo ca nyanga ziŵili ngati mwana wa nkhosa.—Chiv. 13:11
Cifanizilo ca cilombo.—Chiv. 13:15
MAULAMULILO
Ulamulilo wamphamvu padziko lonse wa Britain na America
Bungwe la League of Nations komanso United Nations
Satana Mdyelekezi
Maboma onse otsutsana na Mulungu