LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsa. 4
  • Esau Anagulitsa Udindo Wake Monga Woyamba Kubadwa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Esau Anagulitsa Udindo Wake Monga Woyamba Kubadwa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Yakobo Analandila Coloŵa
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Anthu Auzimu Amapanga Zisankho Zanzelu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
  • Ana Amapasa Osiyana
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 March tsa. 4
M’bale akusinkha-sinkha zimene waŵelenga m’Baibo. Iye akuyelekezela kuti akuona Esau akugulitsa ukulu wake kwa Yakobo mwa kuusinthanitsa na mbale ya mphodza.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 25-26

Esau Anagulitsa Udindo Wake Monga Woyamba Kubadwa

25:27-34

Esau ‘sanayamikile zinthu zopatulika.’ (Aheb. 12:16) Zotulukapo zake, anagulitsa udindo wake monga woyamba kubadwa. Anakwatilanso akazi aŵili amitundu ina.—Gen. 26:34, 35.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ningaonetse bwanji kuti nimayamikila kwambili zinthu zopatulika izi?’

  • Ubale wanga na Yehova

  • Mzimu woyela

  • Kudziŵika na dzina loyela la Yehova

  • Ulaliki

  • Misonkhano yacikhristu

  • Cikwati

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani