LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 July tsa. 4
  • Mose na Aroni aonetsa kulimba kwambili

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mose na Aroni aonetsa kulimba kwambili
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Mose Ndi Aroni Aonana Ndi Farao
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Kodi Mumaona “Wosaonekayo”?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Tsanzilani Cikhulupililo ca Mose
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Mose Amenya Cimwala Ndi Ndodo
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 July tsa. 4
Mose na Aroni aonekela pamaso pa Farao, amene wakhala pa mpando wake wacifumu.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKSODO 10-11

Mose na Aroni Anaonetsa Kulimba Mtima Kwambili

10:3-6, 24-26, 28; 11:4-8

Mose na Aroni anaonetsa kulimba mtima kwambili pokamba na Farao, amene anali munthu wamphamvu kwambili pa dziko lapansi panthawiyo. N’ciani cinawathandiza kucita zimenezo? Pokamba za Mose, Baibo imati: “Mwa cikhulupililo anacoka mu Iguputo, koma osati cifukwa coopa mfumu ayi, pakuti anapitiliza kupilila moleza mtima ngati kuti akuona Wosaonekayo.” (Aheb. 11:27) Mose na Aroni anali na cikhulupililo colimba mwa Yehova ndipo anamudalila.

Kodi ni mikhalidwe iti imene imafuna kulimba mtima kuti tifotokoze za cikhulupililo cathu kwa munthu wa paudindo?

Zithunzi: Zocitika zimene zimafuna kulimba mtima kwathu. 1. Wacicepele kusukulu waimilila mwaulemu pamene anzake acitila saliyuti mbendela. 2. M’bale waimilila pamaso pa nduna za khoti . 3. M’bale wacicepele agaŵila kathilakiti kwa mwininyumba pamene wapolisi ayang’ana capafupi.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani