LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 15
  • Poyamba Sauli Anali Wodzicepetsa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Poyamba Sauli Anali Wodzicepetsa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Kudzikweza Kumanyazitsa Munthu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kumvela Kumaposa Nsembe
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yesu Asankha Saulo
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Davide na Sauli
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 15

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Poyamba Sauli Anali Wodzicepetsa

Sauli anali wodzicepetsa, ndipo anaopa kulandila ufumu (1 Sam. 9:21; 10:20-22; w20.08 10 ¶11)

Sauli sanacite zinthu mopupuluma pamene anthu ena anali kumunenela zoipa (1 Sam. 10:27; 11:12, 13; w14 3/1 9 ¶8)

Sauli analola mzimu woyela wa Yehova kumutsogolela (1 Sam. 11:5-7; w95 12/15 10 ¶1)

Mkulu akuonetsa lemba mlongo amene ali na khadi yoitanila anthu ku cikwati.

Kudzicepetsa kudzatithandiza kuti tiziona maudindo na maluso athu monga mphatso yocokela kwa Yehova. (Aroma 12:3, 16; 1 Akor. 4:7) Komanso ngati ndife odzicepetsa, tidzapitiliza kudalila citsogozo ca Yehova.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani