LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsa. 16
  • Makambilano Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makambilano Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Kumemeza Anthu ku Cikumbutso (March 19–April 15)
  • Ulendo Woyambaa (March 1-18, April 16-30)
  • Ulendo Wobwelelakob
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 March tsa. 16
M’bale na mkazi wake akulandila alendo mwaubwenzi pa Nyumba ya Ufumu.

CITANI KHAMA PA ULALIKI

Makambilano Acitsanzo

Kumemeza Anthu ku Cikumbutso (March 19–April 15)

“Ndife okondwa kukuitanilani ku cocitika capadela kumene kudzapezeka anthu mamiliyoni ambili. Cocitika cimeneci ni mwambo wokumbukila imfa ya Yesu.” Ndiyeno patsani munthuyo kapepala ka ciitanilo kopulinta kapena ka pacipangizo. “Kapepala ka ciitanilo aka kaonetsa nthawi na malo kumene cocitikaci cidzacitikile kwathu kuno [kapena mmene mungalumikizile ku msonkhanowu pa intaneti]. Tikuitanilaninso ku nkhani yapadela imene idzakambidwa kumapeto kwa mlungu woti cikumbutso cicitika mlungu wotsatila.”

Akaonetsa cidwi: Onetsani [kapena tumizani pa meseji kapena pa imelo] vidiyo yakuti Kukumbukila Imfa ya Yesu.

Ulalo: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

Ulendo Woyambaa (March 1-18, April 16-30)

Funso: Kodi Yesu Ndani?

Lemba: Mat. 16:16

Ulalo: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

Ulendo Wobwelelakob

Funso: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

Lemba: Mat. 20:28

Ulalo: Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila nsembe ya dipo la Yesu?

a b Mungasintheko funso na ulalo kuti zigwilizane na mikhalidwe ya kwanuko.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani