CITANI KHAMA PA ULALIKI
Makambilano Acitsanzo
Ulendo Woyambaa
Funso: Tidziŵa bwanji kuti mavuto amene timakumana nawo si cilango cocokela kwa Mulungu?
Lemba: Yak. 1:13
Ulalo: N’cifukwa ciyani timavutika?
Ulendo Wobwelelakob
Funso: N’cifukwa ciyani timavutika?
Lemba: 1 Yoh. 5:19
Ulalo: Kodi Mulungu amamvela bwanji akaona kuti tikuvutika?