LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 10
  • Kulitsani Cikhumbo Canu Cofuna Kucita Cifunilo ca Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kulitsani Cikhumbo Canu Cofuna Kucita Cifunilo ca Mulungu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Davide na Sauli
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Cifukwa Cake Davide Afunikila Kuthaŵa
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Davide Aikidwa Kukhala Mfumu
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Yesu Asankha Saulo
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 10
Zithunzi: 1. Mfumu Sauli modzikuza ikupeleka nsembe pa guwa lansembe. 2. Davide akukana kumwa madzi amene mmodzi wa asilikali ake am’patsa.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kulitsani Cikhumbo Canu Cofuna Kucita Cifunilo ca Mulungu

Cifukwa cakuti Sauli anali wosamvela, Yehova anam’kana (1 Mbiri 10:13, 14)

Yehova anasankha Davide kuti akhale mfumu m’malo mwa Sauli (1 Mbiri 11:3)

Mosiyana na Sauli, Davide analola malamulo a Yehova komanso mfundo zake kum’tsogolela (1 Mbiri 11:15-19; w12 11/15 6 ¶12-13)

Davide anali kukonda kucita cifunilo ca Mulungu. (Sal. 40:8) Ifenso tingakulitse mtima wofuna kucita zoyenela ngati tiphunzila kuona zinthu mmene Yehova amazionela.—Sal. 25:4; w18.06 17 ¶5-6.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani