LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 12
  • Cikondi ca Mulungu Cosasintha Cimatiteteza ku Mabodza a Satana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Cikondi ca Mulungu Cosasintha Cimatiteteza ku Mabodza a Satana
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Cikondi Cosasintha ca Yehova N’ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Mmene Mungakhalile Bwenzi La Mulungu
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Kodi Tingaonetse Bwanji Kuti Yehova Timamukonda?
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Yobu Anakhalabe Wokhulupilika Pamene Anali Kuyesedwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Cikondi ca Mulungu Cosasintha Cimatiteteza ku Mabodza a Satana

Satana amafuna kuti anthu azikhulupilila kuti Yehova ndiye amacititsa zinthu zoipa (Yobu 8:4)

Iye amafuna tiziganiza kuti Yehova alibe nazo kanthu zakuti kaya ndife okhulupilika kwa iye kapena ayi (Yobu 9:​20-22; w15 7/1 12 ¶3)

Cikondi ca Yehova cosasintha cimatiteteza kuti tisasoceletsedwe na mabodza a Satana komanso kuti tikhalebe okhulupilika (Yobu 10:12; Sal. 32:​7, 10; w21.11 6 ¶14)

Mlongo akuganizila na kulemba madalitso osiyanasiyana amene walandila. Tuzithunzi tuonetsa banja lamubweletsela cakudya, mlongo wina akumukumbatila ku Nyumba ya Ufumu, ndiponso akuonelela pulogilamu ya JW Broadcasting.

YESANI KUCITA IZI: Kuti mukhalebe wolimba pokumana na mayeso, ganizilani mmene Yehova akuonetsela cikondi cake cosasintha kwa inu. Kenako lembani zimene mwapeza na kumaziŵelenga kaŵili-kaŵili.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani