LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp24 na. 1 tsa. 16
  • N’kuti Kumene Tingapeze Malangizo Odalilika Masiku Ano?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • N’kuti Kumene Tingapeze Malangizo Odalilika Masiku Ano?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila) —2024
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Ana Anu Adzatumikilabe Yehova Akakula?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
  • Pangani Zosankha Mwanzelu Mukali Acinyamata
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
  • Mmene Ambili Amasankhila Zocita
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila) —2024
  • Baibo Ni Gwelo la Malangizo Odalilika
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila) —2024
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila) —2024
wp24 na. 1 tsa. 16
Mnyamata amene waonetsedwa m’nkhani zapita akuyang’ana pa mapu ataimilila m’njila yopita ku phili. Patsogolo pake pali zikwangwani zambili zolata kosiyana-siyana, ndipo phili likuonekela capatali.

N’kuti Kumene Tingapeze Malangizo Odalilika Masiku Ano?

Popeza zinthu m’dzikoli zikusintha mofulumila, mungatsimikize bwanji kuti zisankho zanu zidzakubweletselani cimwemwe? Mungadziŵe bwanji kuti zinthu zimene zioneka zoyenela masiku ano zidzakhalabe zoyenela m’tsogolo?

Baibo ingakuthandizeni kupanga zisankho zabwino, zimene simudzadandaula nazo m’tsogolo. Kodi zimenezi zingatheke bwanji? Mwa kutsatila malangizo a m’Baibo, imene ni yocokela kwa Mlengi wathu, amene amadziŵa zimene zingatithandize kukhala na cimwemwe ceniceni komanso kukhala otetezeka.

“Iye anakuuza . . . zimene zili zabwino.”—Mika 6:8.

Tingawadalile malangizo anzelu opezeka m’Baibo cifukwa Mawu a Mulungu “ndi odalilika nthawi zonse, kuyambila panopa mpaka kalekale.”—Salimo 111:8.

Fufuzani nokha mmene Baibo ingakuthandizileni m’dzikoli limene likusintha mofulumila.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani