Mfundo ya Kumapeto
^ [1] (ndime 12) Nthawi zina, atumiki a Yehova sakhala na cakudya cokwanila. Kuti mudziŵe cifukwa cake Yehova amalolela kuti zimenezi zicitike, onani nkhani yakuti: “Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi” mu Nsanja ya Mlonda ya September 15, 2014, pa tsamba 22.